2 Samueli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso ayenera kubweza+ nkhosa zinayi+ chifukwa cha kamwana ka nkhosa kakakazi kamene anatenga. Amenewa ndiwo malipiro a zimene wachitazi, pakuti analibe chisoni.”+ Luka 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Zakeyu anaimirira ndi kuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense pomunamizira mlandu+ ndibweza kuwirikiza kanayi.”+
6 Ndiponso ayenera kubweza+ nkhosa zinayi+ chifukwa cha kamwana ka nkhosa kakakazi kamene anatenga. Amenewa ndiwo malipiro a zimene wachitazi, pakuti analibe chisoni.”+
8 Koma Zakeyu anaimirira ndi kuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense pomunamizira mlandu+ ndibweza kuwirikiza kanayi.”+