Ekisodo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Munthu akaba ng’ombe kapena nkhosa, n’kuipha kapena kuigulitsa, azilipira ng’ombe zisanu pa ng’ombe imodzi imene waba, ndi nkhosa zinayi pa nkhosa imodzi imene waba.+ Levitiko 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa. 2 Samueli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso ayenera kubweza+ nkhosa zinayi+ chifukwa cha kamwana ka nkhosa kakakazi kamene anatenga. Amenewa ndiwo malipiro a zimene wachitazi, pakuti analibe chisoni.”+
22 “Munthu akaba ng’ombe kapena nkhosa, n’kuipha kapena kuigulitsa, azilipira ng’ombe zisanu pa ng’ombe imodzi imene waba, ndi nkhosa zinayi pa nkhosa imodzi imene waba.+
5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa.
6 Ndiponso ayenera kubweza+ nkhosa zinayi+ chifukwa cha kamwana ka nkhosa kakakazi kamene anatenga. Amenewa ndiwo malipiro a zimene wachitazi, pakuti analibe chisoni.”+