1 Samueli 25:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako Abigayeli+ ananyamuka mofulumira ndi kukwera pabulu,+ atsikana ake asanu antchito akumutsatira pambuyo. Iye anatsatira nthumwi za Davide ndipo anakakhala mkazi wake.
42 Kenako Abigayeli+ ananyamuka mofulumira ndi kukwera pabulu,+ atsikana ake asanu antchito akumutsatira pambuyo. Iye anatsatira nthumwi za Davide ndipo anakakhala mkazi wake.