2 Samueli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako amuna a ku Yuda+ anabwera ndi kudzoza+ Davide kumeneko kukhala mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Ndiyeno anthu anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli m’manda.” 2 Samueli 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Heburoni analamulira monga mfumu ya Yuda zaka 7 ndi miyezi 6.+ Ku Yerusalemu+ analamulira monga mfumu ya Isiraeli yense ndiponso Yuda zaka 33.
4 Kenako amuna a ku Yuda+ anabwera ndi kudzoza+ Davide kumeneko kukhala mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Ndiyeno anthu anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli m’manda.”
5 Ku Heburoni analamulira monga mfumu ya Yuda zaka 7 ndi miyezi 6.+ Ku Yerusalemu+ analamulira monga mfumu ya Isiraeli yense ndiponso Yuda zaka 33.