Miyambo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+ Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.
23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.