Levitiko 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Mwamuna akatenga mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake, n’kugona naye, chimenecho ndi chinthu chochititsa manyazi.+ Chotero onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo. Iye wavula mlongo wake ndipo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho. Mateyu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+ 1 Atesalonika 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 osati mwa chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ ngati chimene anthu a mitundu ina+ osadziwa Mulungu+ ali nacho.
17 “‘Mwamuna akatenga mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake, n’kugona naye, chimenecho ndi chinthu chochititsa manyazi.+ Chotero onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo. Iye wavula mlongo wake ndipo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.
19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+
5 osati mwa chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ ngati chimene anthu a mitundu ina+ osadziwa Mulungu+ ali nacho.