Deuteronomo 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Ezekieli 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wachita zinthu zonyansa ndi mkazi wa mnzake,+ ndipo munthu wachita khalidwe lotayirira mwa kugona ndi mkazi wa mwana wake.+ Munthu wagona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake.+
22 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
11 Munthu wachita zinthu zonyansa ndi mkazi wa mnzake,+ ndipo munthu wachita khalidwe lotayirira mwa kugona ndi mkazi wa mwana wake.+ Munthu wagona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake.+