1 Samueli 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide ali kuchipululu, anamva kuti Nabala akumeta ubweya+ wa nkhosa zake. 1 Samueli 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ine nditenge mkate wanga,+ madzi ndi nyama imene ndaphera anyamata anga ometa ubweya wa nkhosa n’kupereka kwa amuna amene sindikudziwa m’pang’ono pomwe kumene achokera?”+
11 Ndiye ine nditenge mkate wanga,+ madzi ndi nyama imene ndaphera anyamata anga ometa ubweya wa nkhosa n’kupereka kwa amuna amene sindikudziwa m’pang’ono pomwe kumene achokera?”+