Miyambo 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngakhale azilankhula mawu okoma,+ usam’khulupirire+ chifukwa mumtima mwake muli zinthu 7 zonyansa.+ Miyambo 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chidani chimaphimbidwa ndi chinyengo. Zoipa zake zidzaululika mumpingo.+
25 Ngakhale azilankhula mawu okoma,+ usam’khulupirire+ chifukwa mumtima mwake muli zinthu 7 zonyansa.+