1 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu. 1 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho amuna a mumzinda wake, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzindawo, anachita zimene Yezebeli anawatuma, mogwirizana ndi zimene iye analemba m’makalata amene anawatumizira.+
18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.
11 Choncho amuna a mumzinda wake, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzindawo, anachita zimene Yezebeli anawatuma, mogwirizana ndi zimene iye analemba m’makalata amene anawatumizira.+