-
2 Samueli 13:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Pamapeto pake mfumu Davide inalakalaka kupita kwa Abisalomu, pakuti anali atadzitonthoza pambuyo pa imfa ya Aminoni.
-
-
2 Samueli 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho tsiku limenelo chipulumutso chinasanduka nthawi yoti anthu onse alire maliro, chifukwa tsiku limenelo anthu anamva kuti: “Mfumu yakhumudwa ndi imfa ya mwana wake.”
-