Ekisodo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Moto ukabuka n’kugwirira zomera zaminga, ndipo wafalikira m’munda n’kutentha mitolo yambewu, mbewu zosadula kapena munda wonse,+ amene anayatsa motowo azilipira ndithu chifukwa cha zotenthedwazo. Oweruza 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, n’kutumiza nkhandwezo m’minda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa mpaka minda ya maolivi.+
6 “Moto ukabuka n’kugwirira zomera zaminga, ndipo wafalikira m’munda n’kutentha mitolo yambewu, mbewu zosadula kapena munda wonse,+ amene anayatsa motowo azilipira ndithu chifukwa cha zotenthedwazo.
5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, n’kutumiza nkhandwezo m’minda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa mpaka minda ya maolivi.+