Levitiko 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake+ kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ng’ombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.
21 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake+ kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ng’ombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.