Oweruza 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho abale a mayi ake anayamba kulankhula mawu onsewa nzika zonse za Sekemu zikumva, moti mitima yawo inakonda Abimeleki,+ chifukwa anati: “Ndi m’bale wathu ameneyu.”+
3 Choncho abale a mayi ake anayamba kulankhula mawu onsewa nzika zonse za Sekemu zikumva, moti mitima yawo inakonda Abimeleki,+ chifukwa anati: “Ndi m’bale wathu ameneyu.”+