2 Samueli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pambuyo pake Husai anauza Zadoki+ ndi Abiyatara ansembe, kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo kwa Abisalomu ndi akulu a Isiraeli ndipo wanena zakutizakuti, koma malangizo amene ine ndapereka, ndanena zakutizakuti.
15 Pambuyo pake Husai anauza Zadoki+ ndi Abiyatara ansembe, kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo kwa Abisalomu ndi akulu a Isiraeli ndipo wanena zakutizakuti, koma malangizo amene ine ndapereka, ndanena zakutizakuti.