2 Samueli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi. 2 Samueli 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kodi kumeneko suli ndi Zadoki ndi Abiyatara ansembe?+ Chilichonse chimene ukamve kuchokera kunyumba ya mfumu ukauze Zadoki ndi Abiyatara ansembe.+ 1 Mbiri 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Panalinso Zadoki+ mnyamata wamphamvu ndi wolimba mtima ndi atsogoleri 22 a m’nyumba ya makolo ake.
17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi.
35 Kodi kumeneko suli ndi Zadoki ndi Abiyatara ansembe?+ Chilichonse chimene ukamve kuchokera kunyumba ya mfumu ukauze Zadoki ndi Abiyatara ansembe.+
28 Panalinso Zadoki+ mnyamata wamphamvu ndi wolimba mtima ndi atsogoleri 22 a m’nyumba ya makolo ake.