2 Samueli 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yowabu atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kudalitsa mfumu,+ n’kunena kuti: “Lero ndadziwa kuti ine mtumiki wanu mwandikomera mtima,+ mbuyanga mfumu, chifukwa chakuti inu mfumu mwamvera mawu anga ine mtumiki wanu.”
22 Yowabu atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kudalitsa mfumu,+ n’kunena kuti: “Lero ndadziwa kuti ine mtumiki wanu mwandikomera mtima,+ mbuyanga mfumu, chifukwa chakuti inu mfumu mwamvera mawu anga ine mtumiki wanu.”