Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”

  • 1 Samueli 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma poyankha Davide analumbira+ kuti: “Bambo ako ayenera kuti akudziwa ndithu kuti iweyo umandikonda.+ Pa chifukwa chimenechi iwo adzanena kuti, ‘Musamuuze zimenezi Yonatani kuti zingamupweteketse mtima.’ Moti ndikunenetsa, pali Yehova Mulungu wamoyo,+ komanso pali moyo wako,+ imfa ili pafupi kwambiri ndi ine!”+

  • Esitere 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ngati mungandikomere mtima mfumu+ ndipo ngati zingakukomereni kuchita zimene ndapempha n’kundipatsa zimene ndikufuna, inu mfumu ndi Hamani mubwere kuphwando limene ndidzakukonzerani mawa. Ndipo mawa ndidzanena pempho langa monga mmene inu mfumu mwanenera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena