Genesis 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Patapita nthawi, Abimeleki anafika kwa iye kuchokera ku Gerari. Anafika limodzi ndi Ahuzati bwenzi lake lapamtima, komanso Fikolo mkulu wa asilikali ake.+ 1 Mafumu 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Azariya mwana wa Natani+ anali mkulu wa nduna, ndipo Zabudu mwana wa Natani anali wansembe, bwenzi+ la mfumu. Miyambo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse,+ ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.+ Miyambo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+
26 Patapita nthawi, Abimeleki anafika kwa iye kuchokera ku Gerari. Anafika limodzi ndi Ahuzati bwenzi lake lapamtima, komanso Fikolo mkulu wa asilikali ake.+
5 Azariya mwana wa Natani+ anali mkulu wa nduna, ndipo Zabudu mwana wa Natani anali wansembe, bwenzi+ la mfumu.
17 Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse,+ ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.+
24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+