Rute 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kumene inu mudzafere inenso ndidzafera komweko,+ ndipo ndidzaikidwanso komweko. Yehova andilange kwambiri+ ngati chinachake kupatulapo imfa chingandilekanitse ndi inu.” 1 Samueli 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Yonatani, mwana wa Sauli, anali kukonda kwambiri Davide.+ Choncho Yonatani anauza Davide kuti: “Sauli, bambo anga, akufuna kukupha. Chonde, mawa m’mawa ukhale wosamala. Ukakhale pamalo obisika ndipo ukabisalebe choncho.+ 2 Samueli 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.
17 Kumene inu mudzafere inenso ndidzafera komweko,+ ndipo ndidzaikidwanso komweko. Yehova andilange kwambiri+ ngati chinachake kupatulapo imfa chingandilekanitse ndi inu.”
2 Koma Yonatani, mwana wa Sauli, anali kukonda kwambiri Davide.+ Choncho Yonatani anauza Davide kuti: “Sauli, bambo anga, akufuna kukupha. Chonde, mawa m’mawa ukhale wosamala. Ukakhale pamalo obisika ndipo ukabisalebe choncho.+
28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.