Genesis 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Abulahamu anathamangira kwa Sara n’kumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu ya seya,* uukande, ndipo upange makeke ozungulira.”+ 1 Samueli 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano mkaziyo anali ndi mwana wa ng’ombe wonenepa+ m’nyumba yake. Choncho anam’pereka nsembe msangamsanga,+ ndipo anatenga ufa n’kuukanda ndi kuphika mikate yopanda chofufumitsa.
6 Chotero Abulahamu anathamangira kwa Sara n’kumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu ya seya,* uukande, ndipo upange makeke ozungulira.”+
24 Tsopano mkaziyo anali ndi mwana wa ng’ombe wonenepa+ m’nyumba yake. Choncho anam’pereka nsembe msangamsanga,+ ndipo anatenga ufa n’kuukanda ndi kuphika mikate yopanda chofufumitsa.