Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+

  • 2 Samueli 1:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,

      Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+

      Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+

  • Miyambo 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+

  • Yohane 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena