1 Mafumu 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira. 2 Mbiri 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yerobowamu+ mwana wa Nebati atamva zimenezi ali ku Iguputo,+ (pajatu anathawa mfumu Solomo,) nthawi yomweyo anabwerera kuchokera ku Iguputoko.+
40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira.
2 Yerobowamu+ mwana wa Nebati atamva zimenezi ali ku Iguputo,+ (pajatu anathawa mfumu Solomo,) nthawi yomweyo anabwerera kuchokera ku Iguputoko.+