Amosi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ pakuti ndi malo opatulika a mfumu,+ ndiponso Beteli ndi nyumba ya ufumu uno.”
13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ pakuti ndi malo opatulika a mfumu,+ ndiponso Beteli ndi nyumba ya ufumu uno.”