Amosi 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Koma inu munapitiriza kupatsa Anaziri vinyo kuti amwe+ ndipo aneneri munawalamula kuti: “Musamanenere.”+ Machitidwe 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komabe, kuti nkhaniyi isapitirire kufalikira kwa anthu ena, tiyeni tiwaopseze kuti asalankhulenso m’dzina limeneli kwa munthu wina aliyense.”+ Machitidwe 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu+ kuti musadzaphunzitsenso m’dzina limeneli, koma taonani tsopano! Mwadzaza Yerusalemu yense ndi chiphunzitso chanuchi,+ ndipo mwatsimikiza mtima ndithu kuti mubweretse magazi+ a munthu ameneyu pa ife.”
12 “‘Koma inu munapitiriza kupatsa Anaziri vinyo kuti amwe+ ndipo aneneri munawalamula kuti: “Musamanenere.”+
17 Komabe, kuti nkhaniyi isapitirire kufalikira kwa anthu ena, tiyeni tiwaopseze kuti asalankhulenso m’dzina limeneli kwa munthu wina aliyense.”+
28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu+ kuti musadzaphunzitsenso m’dzina limeneli, koma taonani tsopano! Mwadzaza Yerusalemu yense ndi chiphunzitso chanuchi,+ ndipo mwatsimikiza mtima ndithu kuti mubweretse magazi+ a munthu ameneyu pa ife.”