Salimo 78:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene analikonda.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+