1 Mafumu 8:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.” 2 Mbiri 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma malo okwezeka+ analipobe mu Isiraeli.+ Ngakhale zinali choncho, mtima wa Asa unali wathunthu masiku ake onse.+
61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.”
17 Koma malo okwezeka+ analipobe mu Isiraeli.+ Ngakhale zinali choncho, mtima wa Asa unali wathunthu masiku ake onse.+