Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo nawonso anapitiriza kudzimangira malo okwezeka,+ zipilala zopatulika,+ ndi mizati yopatulika+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali,+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+

  • 2 Mafumu 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+

  • 2 Mafumu 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chotero iye anapha ansembe onse+ a m’malo okwezeka n’kuwapereka nsembe pamaguwa ansembe kumeneko. Kenako anawotcha mafupa a anthu pamaguwa ansembewo.+ Atatero anabwerera ku Yerusalemu.

  • Ezekieli 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Unene kuti, ‘Inu mapiri a Isiraeli, imvani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa:+ Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kwa mapiri, zitunda,+ mitsinje ndi zigwa: “Ine ndidzakubweretserani lupanga ndipo ndidzawononga malo anu okwezeka.+

  • Ezekieli 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Unatenga zovala zako zina n’kupangira malo okwezeka+ okhala ndi mitundu yosiyanasiyana ndipo unayamba kuchitirapo uhule.+ Zoterezi siziyenera kuchitika. Zisamachitike ayi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena