2 Mafumu 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inagwetsanso nyumba za mahule achimuna a pakachisi+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, mmene akazi anali kulukiramo akachisi a mahema a mzati wopatulika. Ezekieli 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense akunyada chifukwa cha chinthu chake chokongoletsera. Iwo agwiritsira ntchito siliva ndi golide kupangira mafano awo onyansa,+ ndi zinthu zawo zonyansa.+ N’chifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzaipidwe nazo.+
7 Inagwetsanso nyumba za mahule achimuna a pakachisi+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, mmene akazi anali kulukiramo akachisi a mahema a mzati wopatulika.
20 Aliyense akunyada chifukwa cha chinthu chake chokongoletsera. Iwo agwiritsira ntchito siliva ndi golide kupangira mafano awo onyansa,+ ndi zinthu zawo zonyansa.+ N’chifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzaipidwe nazo.+