Levitiko 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musadzipangire milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika. Musaike mwala wokhala ndi zithunzi zojambula mochita kugoba+ m’dziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu. 2 Mafumu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati mmene anachitira bambo ake+ kapenanso mmene anachitira mayi ake. Iye anachotsa chipilala chopatulika+ cha Baala chimene bambo ake anapanga.+
26 “‘Musadzipangire milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika. Musaike mwala wokhala ndi zithunzi zojambula mochita kugoba+ m’dziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.
2 Iye anali kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati mmene anachitira bambo ake+ kapenanso mmene anachitira mayi ake. Iye anachotsa chipilala chopatulika+ cha Baala chimene bambo ake anapanga.+