2 Mbiri 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno mfumu Asa inatenga Ayuda onse,+ ndipo iwo anapita kukatenga miyala ya ku Rama+ ndi matabwa ake, zimene Basa ankamangira.+ Mfumuyo inatenga zinthu zimenezo n’kuyamba kukamangira Geba+ ndi Mizipa.+
6 Ndiyeno mfumu Asa inatenga Ayuda onse,+ ndipo iwo anapita kukatenga miyala ya ku Rama+ ndi matabwa ake, zimene Basa ankamangira.+ Mfumuyo inatenga zinthu zimenezo n’kuyamba kukamangira Geba+ ndi Mizipa.+