2 Mbiri 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’chaka cha 39 cha ulamuliro wa Asa, iye anadwala nthenda ya mapazi+ mpaka matendawo anakula kwambiri. Koma ngakhale pamene anali kudwala, iye anafunafuna ochiritsa+ osati Yehova.+ Mlaliki 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kumbukira Mlengi wako Wamkulu+ masiku a unyamata wako,+ asanafike masiku oipa+ komanso zisanafike zaka zimene udzati: “Moyo sukundisangalatsa.”+
12 M’chaka cha 39 cha ulamuliro wa Asa, iye anadwala nthenda ya mapazi+ mpaka matendawo anakula kwambiri. Koma ngakhale pamene anali kudwala, iye anafunafuna ochiritsa+ osati Yehova.+
12 Kumbukira Mlengi wako Wamkulu+ masiku a unyamata wako,+ asanafike masiku oipa+ komanso zisanafike zaka zimene udzati: “Moyo sukundisangalatsa.”+