Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 71:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+

      Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+

  • Salimo 110:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+

      Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+

      Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+

  • Salimo 148:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu anyamata+ ndi inunso anamwali,+

      Inu okalamba+ pamodzi ndi ana.+

  • Luka 2:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Koma iye anawayankha kuti: “Mumandifunafuna chifukwa chiyani? Kodi simunadziwe kuti ndiyenera kupezeka m’nyumba ya Atate wanga?”+

  • 2 Timoteyo 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena