Salimo 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Adzamubweretsa kwa mfumu atavala chovala choluka.+Anamwali anzake omuperekeza akubwera nawo kwa iwe.+ Machitidwe 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwamuna ameneyu anali ndi ana aakazi anayi, anamwali, amene anali kunenera.+
14 Adzamubweretsa kwa mfumu atavala chovala choluka.+Anamwali anzake omuperekeza akubwera nawo kwa iwe.+