Nyimbo ya Solomo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi+ ndiponso pali mphoyo+ zakutchire, kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.+ Nyimbo ya Solomo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+ Nyimbo ya Solomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi wachikondi wako wapita kuti, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako walowera kuti, kuti tikuthandize kum’funafuna?”
7 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi+ ndiponso pali mphoyo+ zakutchire, kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.+
9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+
6 “Kodi wachikondi wako wapita kuti, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako walowera kuti, kuti tikuthandize kum’funafuna?”