Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+ 2 Mafumu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawiyi, Hezekiya anafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro chakuti Yehova andichiritsa, ndi kuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu n’chiyani?”+ Salimo 103:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+
8 Pa nthawiyi, Hezekiya anafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro chakuti Yehova andichiritsa, ndi kuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu n’chiyani?”+