Yoswa 19:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Eliteke, Gebetoni,+ Baalati,+ Yoswa 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuchokera m’fuko la Dani, anawapatsa Eliteke ndi malo ake odyetserako ziweto, Gebetoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mafumu 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’chaka cha 27 cha Asa mfumu ya Yuda, Zimiri anakhala mfumu ku Tiriza kwa masiku 7.+ Pa nthawiyo anthu anali atamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gebetoni,+ umene unali wa Afilisiti, kuti authire nkhondo.
23 Kuchokera m’fuko la Dani, anawapatsa Eliteke ndi malo ake odyetserako ziweto, Gebetoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
15 M’chaka cha 27 cha Asa mfumu ya Yuda, Zimiri anakhala mfumu ku Tiriza kwa masiku 7.+ Pa nthawiyo anthu anali atamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gebetoni,+ umene unali wa Afilisiti, kuti authire nkhondo.