Yoswa 19:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Eliteke, Gebetoni,+ Baalati,+ Yoswa 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuchokera m’fuko la Dani, anawapatsa Eliteke ndi malo ake odyetserako ziweto, Gebetoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mafumu 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno Basa+ mwana wa Ahiya wa nyumba ya Isakara, anayamba kuchitira chiwembu Nadabu. Iye anapha Nadabu kumzinda wa Gebetoni,+ womwe unali m’manja mwa Afilisiti, pa nthawi imene Nadabu ndi Aisiraeli onse anali kuukira Gebetoni.
23 Kuchokera m’fuko la Dani, anawapatsa Eliteke ndi malo ake odyetserako ziweto, Gebetoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
27 Ndiyeno Basa+ mwana wa Ahiya wa nyumba ya Isakara, anayamba kuchitira chiwembu Nadabu. Iye anapha Nadabu kumzinda wa Gebetoni,+ womwe unali m’manja mwa Afilisiti, pa nthawi imene Nadabu ndi Aisiraeli onse anali kuukira Gebetoni.