1 Mafumu 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Basa atangomva zimenezi, nthawi yomweyo anasiya kumanga Rama+ ndipo anapitiriza kukhala ku Tiriza.+ 1 Mafumu 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 M’chaka chachitatu cha Asa mfumu ya Yuda, Basa mwana wa Ahiya anakhala mfumu ya Isiraeli yense ku Tiriza kwa zaka 24.+
21 Basa atangomva zimenezi, nthawi yomweyo anasiya kumanga Rama+ ndipo anapitiriza kukhala ku Tiriza.+
33 M’chaka chachitatu cha Asa mfumu ya Yuda, Basa mwana wa Ahiya anakhala mfumu ya Isiraeli yense ku Tiriza kwa zaka 24.+