1 Mafumu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atamva zimenezi, mkazi wa Yerobowamu ananyamuka n’kumapita ndipo anafika ku Tiriza.+ Atangofika pakhomo la nyumba yawo, mnyamatayo anamwalira. Nyimbo ya Solomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Wokondedwa wangawe, ndiwe wokongola+ ngati Mzinda Wosangalatsa.+ Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+ ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali+ amene azungulira mbendera.+
17 Atamva zimenezi, mkazi wa Yerobowamu ananyamuka n’kumapita ndipo anafika ku Tiriza.+ Atangofika pakhomo la nyumba yawo, mnyamatayo anamwalira.
4 “Wokondedwa wangawe, ndiwe wokongola+ ngati Mzinda Wosangalatsa.+ Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+ ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali+ amene azungulira mbendera.+