Genesis 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Abulahamu anathamangira kwa Sara n’kumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu ya seya,* uukande, ndipo upange makeke ozungulira.”+
6 Chotero Abulahamu anathamangira kwa Sara n’kumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu ya seya,* uukande, ndipo upange makeke ozungulira.”+