2 Mafumu 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Elisa anamuyankha kuti: “Ndiye ndikuchitire chiyani?+ Tanena, uli ndi chiyani m’nyumba mwako?” Mayiyo anayankha kuti: “Ine kapolo wanu ndilibe chilichonse m’nyumba mwanga, ndili ndi kamtsuko ka mafuta kokha basi.”+
2 Ndiyeno Elisa anamuyankha kuti: “Ndiye ndikuchitire chiyani?+ Tanena, uli ndi chiyani m’nyumba mwako?” Mayiyo anayankha kuti: “Ine kapolo wanu ndilibe chilichonse m’nyumba mwanga, ndili ndi kamtsuko ka mafuta kokha basi.”+