Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Agalatiya 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ngati tingathe,+ tiyeni tichitire onse zabwino, koma makamaka abale ndi alongo athu m’chikhulupiriro.+ Aheberi 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
10 Chotero ngati tingathe,+ tiyeni tichitire onse zabwino, koma makamaka abale ndi alongo athu m’chikhulupiriro.+
16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+
27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+