Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+

  • 2 Samueli 19:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma Davide anati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya kuti lero mukhale otsutsana+ nane? Kodi mu Isiraeli muyenera kuphedwa munthu aliyense lero?+ Kodi ine sindikudziwa bwino kuti lero ndine mfumu ya Isiraeli?”

  • 2 Mafumu 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Elisa anafunsa mfumu ya Isiraeli kuti: “Ndili nanu chiyani?+ Pitani kwa aneneri+ a bambo anu ndi kwa aneneri a mayi anu.” Koma mfumu ya Isiraeliyo inati: “Ayi musatero, chifukwa Yehova wasonkhanitsa ife mafumu atatu kuti atipereke m’manja mwa Mowabu.”+

  • Mateyu 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+

  • Maliko 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera+ wa Mulungu.”+

  • Yohane 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma Yesu anauza mayi akewo kuti: “Kodi ndili nanu chiyani mayi?+ Nthawi yanga sinafike.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena