Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 17:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.”

  • Luka 4:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+

  • Luka 4:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri.+ Zinali kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana+ wa Mulungu.” Koma iye anali kudzudzula ziwandazo, ndipo sanali kuzilola kuti zilankhule,+ chifukwa zinali kudziwa kuti iye+ ndi Khristu.+

  • Luka 8:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ataona Yesu anafuula kwambiri ndi kudzigwetsa pansi pamaso pake. Kenako anafuula ndi mawu amphamvu kuti: “Kodi ndili nanu chiyani,+ Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba? Chonde, chonde, musandizunze.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena