Mateyu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+ Maliko 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhalenso mizimu yonyansa,+ imati ikamuona, inali kudzigwetsa pansi pamaso pake ndi kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.”+
29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+
11 Ngakhalenso mizimu yonyansa,+ imati ikamuona, inali kudzigwetsa pansi pamaso pake ndi kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.”+