Maliko 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndipo atafuula ndi mawu amphamvu,+ anati: “Kodi ndili nanu chiyani, Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba?+ Ndikukulumbiritsani+ pali Mulungu kuti musandizunze.”+ Luka 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri.+ Zinali kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana+ wa Mulungu.” Koma iye anali kudzudzula ziwandazo, ndipo sanali kuzilola kuti zilankhule,+ chifukwa zinali kudziwa kuti iye+ ndi Khristu.+
7 ndipo atafuula ndi mawu amphamvu,+ anati: “Kodi ndili nanu chiyani, Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba?+ Ndikukulumbiritsani+ pali Mulungu kuti musandizunze.”+
41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri.+ Zinali kufuula kuti: “Inu ndinu Mwana+ wa Mulungu.” Koma iye anali kudzudzula ziwandazo, ndipo sanali kuzilola kuti zilankhule,+ chifukwa zinali kudziwa kuti iye+ ndi Khristu.+