1 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.” Yakobo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho?+ Ukuchita bwino. Koma ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+
18 Mayiyo ataona zimenezi, anauza Eliya kuti: “Ndili nanu chiyani+ inu munthu wa Mulungu woona? Mwabwera kwa ine kudzandikumbutsa cholakwa changa+ ndi kudzapha mwana wanga.”
19 Umakhulupirira kuti kuli Mulungu mmodzi, si choncho?+ Ukuchita bwino. Koma ziwanda nazonso zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera.+