Luka 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa lero wakubadwirani Mpulumutsi,+ amene ndi Khristu Ambuye,+ mumzinda wa Davide.+ Luka 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+
34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+