Mateyu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+ Luka 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ataona Yesu anafuula kwambiri ndi kudzigwetsa pansi pamaso pake. Kenako anafuula ndi mawu amphamvu kuti: “Kodi ndili nanu chiyani,+ Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba? Chonde, chonde, musandizunze.”+
29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+
28 Ataona Yesu anafuula kwambiri ndi kudzigwetsa pansi pamaso pake. Kenako anafuula ndi mawu amphamvu kuti: “Kodi ndili nanu chiyani,+ Yesu, Mwana wa Mulungu Wam’mwambamwamba? Chonde, chonde, musandizunze.”+